JM P.O.P COMPANY

JM P.O.P COMPANY Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from JM P.O.P COMPANY, Home decor, Mtandire, Lilongwe.
(1)

We are professional p.o.p work and interior design company based in Lilongwe, Malawi 🇲🇼

Our services ✨️

✔️Ceiling Design ✔️Roofing ✔️p.o.p design ✔️Painting ✔️Blundering ✔️Electric & etc

Quotation for free 📲+265 999286474

Payment 💰 (NB)1010523342

10/08/2026
Ine nde dolo pa nkhani yopanga plaster of paris (pop) ndipo palibeso wina angandipo tandipaseni ntchito zanuzo kuti mudz...
09/08/2026

Ine nde dolo pa nkhani yopanga plaster of paris (pop) ndipo palibeso wina angandipo tandipaseni ntchito zanuzo kuti mudzazionere Nokha zomwe ndukambazi.🤝🔥🇲🇼🏠

Ndife anamatetule pa nkhani yopanga plaster of paris (p.o.p) nanuso tatitengeni ife kuti tikakungwirireni ntchito zabwin...
07/08/2026

Ndife anamatetule pa nkhani yopanga plaster of paris (p.o.p) nanuso tatitengeni ife kuti tikakungwirireni ntchito zabwino komaso yolimba.🌟✨

Ntchito zabwino  , Ntchito zolimba , Ntchito zotsika mtengo , Anu Ake opanga nde ndifeyo a JM P.O.P COMPANY Mukasakha if...
07/08/2026

Ntchito zabwino , Ntchito zolimba , Ntchito zotsika mtengo , Anu Ake opanga nde ndifeyo a JM P.O.P COMPANY Mukasakha ife ndekuti mwasakha anthu oyenera ndipo simudzapanga regret. Tili Ku Lilongwe koma kulikose timapita mukatiyitana .🏠🤝🇲🇼

Call or WhatsApp number +265 999 28 64 74
Tapangani chisankho chanu lero.

Tafika kale pa Munda kuti tisake ndalama nanga inu muli kuti🤣🤭
07/08/2026

Tafika kale pa Munda kuti tisake ndalama nanga inu muli kuti🤣🤭

07/08/2026

Lero ndi tsiku loyamba lomwe tikuyamba new project yathu Ku Lilongwe chaku Airwing takharani pomwepo tiyendere limodzi 💪🏠🤝🇲🇼🔥

Address

Mtandire
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when JM P.O.P COMPANY posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category