Kias Dreamy Delight Bistro

Kias Dreamy Delight Bistro Where every bite feels like home

Ntcheu Ladies are you ready!!!kias Dreamy Delight Bistro yakubweretserani maphunziro azophikaphika omwe adzayambe pa 21-...
18/02/2026

Ntcheu Ladies are you ready!!!

kias Dreamy Delight Bistro yakubweretserani maphunziro azophikaphika omwe adzayambe pa 21-22 march 2026..

pa tsikuli mudzaphinzira ku baker birthday cake, sausage, pizza,KFC Chicken ,samoosa, doughnut, Salads ,jam/Mango Archer, Biscuits komanso Coated Fish..

zonsezi mudzaphunzira pa mtengo wa k25,000 okha basi , registration fee ndi k10,000 ndipo tsiku lodzayamba kuphunzira mudzabweretsa k15,000 yomwe ikupanga k25,000...

pomaliza mukuyenera kudzagula pamphlet yomwe muli ma recipe a zonse zomwe mwa phunzira pa mtengo wa k5000 ,koma anthu 10 oyambirira kupanga register adzagula pamphlet pa mtengo wa k2,500..

registration yayambiko ndipo tsiku lomaliza kupanga register ndipa 15 march 2026 ...

khalani mzimai otsogola kudziwa ntchito za manja ndikumapindula nazo

Food Making training
18/02/2026

Food Making training

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kias Dreamy Delight Bistro posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share