22/04/2026
Nkhani yabwino kwa ma kasitomala athu!
Sopano tayamba kumapezeka ndi ma solar home system oti mukhonza kugwilisanso ntchito TV (24, 32 and 43 inch).
Mitengo yake ili motele ma complete set
1. 24 inch TV and solar system = K1,365,000
2. 32 inch TV and Solar system = K1,565,000
3. 43inch TV and solar system = K2,238,000
Tipaseni order lero ndipo katundu wanu apezeka mmasiku atatu basi.
Shop yathu ili mu Limbe pafupi ndi Illovo round about opposite pamene panali waterboard yakale.
Tiyimbileni kapena titumizileni uthenga pa whatsapp number 0994 76 63 66