Chilungamo Online

Chilungamo Online Provides practical training in baking, food processing, soap making, and entrepreneurship.

We empower people with skills, business knowledge, and income-generating opportunities to help communities become self-reliant

WhatsApp us +265986795267

Agulu writeπŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡MBALI YAKUNO AGULU πŸ’ƒπŸ’ƒπŸ’ƒKa flour ka K1,000 ndapanga ma donuts 20 😍πŸ₯³ Zomwera tea zamawa zatheka kale! πŸ˜‚β˜•Mene ...
04/09/2026

Agulu writeπŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡

MBALI YAKUNO AGULU πŸ’ƒπŸ’ƒπŸ’ƒ

Ka flour ka K1,000 ndapanga ma donuts 20 😍πŸ₯³ Zomwera tea zamawa zatheka kale! πŸ˜‚β˜•

Mene ndinapangira πŸ‘‡πŸ‘‡

Ndinatenga flour, mchere, yeast, sugar, baking powder ndi cinnamon n’kupanga mix. Kenako ndinathiramo mafuta ophikira pang’ono.

Ndinayamba kuthira madzi ofunda pang’onopang’ono, ndikukanda mpaka dough yanga inalimba bwino komanso kusiya kumata m’manja.

Ndinasiya kuti ifufume kwa 30 minutes, kenako ndinapanga ma shape a donuts. Ndinadikiranso kanthawi kuti afufume pang’ono, kenako ndinawaphika m’mafuta. πŸ˜‹πŸ”₯

K1,000 yokha β†’ ma donuts 20! πŸ₯³πŸ’ƒ

Nanu tayesani kupanga agulu amunawo apume kugula bread πŸ˜†πŸ˜†πŸ˜†πŸ˜‚

Cake done by Violet Mapanga Kameni  One of agulu team Inu muzaphunzira liti agulu πŸ˜†?
04/09/2026

Cake done by Violet Mapanga Kameni

One of agulu team

Inu muzaphunzira liti agulu πŸ˜†?

04/09/2026

🚨 OSAPHONYA TRAINING IYI AGULU! 🚨

🧼 SOAP & GLYCERIN MAKING TRAINING

πŸ“… 7–9 September
⏰ 7:30 PM
πŸ’° K5,000 ONLY!
πŸ“± WhatsApp Group

Muphunzira kupanga:
βœ… Bar Soap
βœ… Pine Gel
βœ… Dishwash
βœ… Hair Shampoo
βœ… Komba (Vaseline)
βœ… Glycerine

πŸ”₯ Mwayiwu musauphonye! Zinthu zimenezi m***a kuyamba kupanga ndi kugulitsa ngati business.

⚠️ Tikufuna anthu ochepa kuti aliyense azapangidwe attend be first to register.

πŸ‘‰ Register now: 0986795267 or 0882400381

πŸ‘‡ Payment details & joining link zili mu comment section.

MILKY ICE BLOCKS RECIPE WITH Chilungamo Online Agulu dziwani kuti freezers uyuyu ndi uja akumayenda malonda town uja  nd...
04/09/2026

MILKY ICE BLOCKS RECIPE WITH Chilungamo Online

Agulu dziwani kuti freezers uyuyu ndi uja akumayenda malonda town uja ndipo ndi ujayo ndidanakamba zoti tikupasira recipe yake ndipo ndiokoma kwambiri.

Mukafuna pdf ya ma recipe ya freezers ilipo only 3000 kwacha
WhatsApp us now 0986795267

Tiyeni tipange milky ice blockyi πŸ˜†

ZOFUNIKIRA

- Madzi otentha β€” 10 Litres
- Shuga β€” 1 Kg (woyera kapena brown)
- Ellis Brown kapena Cremora β€” 375 g
- Vanilla essence β€” 2 tablespoons
- Food colouring β€” mwakufuna kwanu

MMENE MUNGAPANGIRE

1. Ikani madzi otentha okwana 10 litres mu pail yoyera bwino.

2. Thirani Ellis Brown kapena Cremora m'madzi otenthawo, kenako sakanizani bwino mpaka ufa usungunuke kwathunthu.

3. Thirani shuga ndipo sakanizaninso mpaka shuga asungunuke kwathunthu.

4. Siyani zosakanizawo kuti zizire.

5. Mukazizira, onjezerani vanilla essence ndikusakaniza bwino.

6. Gawani zosakanizawo magawo 3 or 4 zofanana malinga ndi ma colour anu.

7. Ikani food colouring yomwe mukufuna m'mbale iliyonse. M***a kugwiritsa ntchito mitundu yosiyanasiyana malinga ndikukonda kwanu.

8. Thirani zosakanizawo plastic paper a ice block kapena mould.

9. Mangani bwino ndipo ikani mu fridge mpaka abwere ice kwambiri.

NB:Musathire vanilla essence ndi food colouring pamene madzi osakanizawo akadali otentha kwambiri. Dikirani kuti uzizire pang'ono kuti flavour ndi colour zikhale bwino.

Inu tayesa lero with ma measurements ochepa mutiuze ma results pano .
Ngati Pali funso ikani ku comment section πŸ‘‡ or ndemanga

Remember training ya soap and glycerin making ilipo pa 7 September bwerani kuti mupeze Malo Anu ntengo ndi 5000 kwacha yokha bas

WhatsApp us now 0986795267 tikupangeni add ku group

Or use link in comment section to join kapena Dinan button la whatssaplo mutipeza mwachangu πŸ‘‡πŸ‘‡

Inu tabwerani muphunzireko kwa ife pa 7 September pano training yomwe ikhodza kusitha moyo wanu only with 5000 kwacha

Share the post and tag your friends kuti aone nawo komaso follow the page chilungamo online

I was reading some important business ideas on the Facebook ukkhudza za ma youth then I meet with this post by young MP ...
04/09/2026

I was reading some important business ideas on the Facebook ukkhudza za ma youth then I meet with this post by young MP called Tony Anjiba Fletcher akuti adatenga achinyamata from his constituency kupita nawo ku Tanzania kuti akaone mene katundu amakhalira and he write πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡

Ndinapita kukatenga ambulance nde ndinatenga achinyamata 4 ku constituency kuti akaphunzire mmene anzathu amapangila business ku Tanzania. Awona kuti ku Tanzania kulibe Ulesi, Ndipo anali odabwa kuti Sanawone munthu atalezera mowa mmamawa, kapena masana, anthu onse anali busy kuthamangitsa ma files.
Anthu akulimbira kunjaku, kuthandiza Boma kuti zinthu ziziyenda mudziko.

Aziwa mitengo ya zinthu ngati izi,
1. Ma spare parts a njinga, aziwa kuti ali pa bwanji.
2. Awona mitengo ya zovala mitundu yonse ndi snapato or ma silipasi.
3. Aziwa mmene mateyara a galimoto amatchipila ndi mateyala anjinga za moto:
4. Awonanso katundu wambiri mmene amatchipila.
5. Aziwanso mitengo ya zinthu zamagetsi monda ma sockets ndi zina zotero mmene zimatchipila.

Katundu yense omwe amagulutsidwa kuno amuwona Ndipo awona kuti, kukatenga katundu ku Tz wina aliyense kuzagulitsa kuno ku Malawi ndi business yosadula.

Ndi MK 750,000.00 Ndekuti ndipogona ndi mayendedwe a Munthu mmodzi,
Kenako kukhala ndi ka 1 million kowodera Ndekuti zatheka pamenepo. Kukhala ndi 3million Ndekuti Iweyo uli bwino kwambiri.

Anthu 4 atalandira za give zija, ndikumupatsa munthu mmodzi kuti azawode ngati kuti onse ayika ma shares Ndekuti anthu amenewa akhala ndi shop yogulisa zovala kapena nsapato or ma jersey ampira or ma spares a njinga zamoto mu Cz.

Nkhani ndi yakuti, kukawoda ku Tanzania si business yodula, ndi business yabwino kwambiri Ndipo munthu utha kuchita bwino mwachangu.

NB:Pano sitipanga za ndale koma kutenga zofunikirazo bas I like zomwe walemba komaso ma business ideas

Big up to Hourable πŸ™

Our student tried this swan freezers  from last week training Akuoneka kumeneko?
04/09/2026

Our student tried this swan freezers from last week training

Akuoneka kumeneko?

Agulu write Kuyesa yesaThis freezers is from our student from last week training ya freezers and ice cream Akuoneka kume...
03/09/2026

Agulu write

Kuyesa yesa

This freezers is from our student from last week training ya freezers and ice cream

Akuoneka kumeneko agulu koma?

Ma set clean and smart inu

Remember training ya soap and glycerin ilipo pa 7 September

Register now 0986795267

Agulu write Testing testing ngakhale kamangidwe kativutaπŸ™„πŸ€£ Iyiyi ndi feedback ya class  yomwe tidapanga osayiwara Well d...
03/09/2026

Agulu write

Testing testing ngakhale kamangidwe kativutaπŸ™„πŸ€£


Iyiyi ndi feedback ya class yomwe tidapanga osayiwara

Well done agulu

SOAP AND GLYCERIN MAKING TRAINING Tikumane  pa 7 September muphunzire kapangidwe kaBar Soap Pine gel wokoloperaDishwashH...
03/09/2026

SOAP AND GLYCERIN MAKING TRAINING

Tikumane pa 7 September muphunzire kapangidwe ka

Bar Soap
Pine gel wokolopera
Dishwash
Hair Shampoo
Komba (Vaseline)
Glycerine

Zonsezi kuphunzira ndi 5,000 basi

Tsiku :pa 7 September mpaka pa 9 September

Fees :5000 kwacha bas
Nthawi 7:30 pm

Uku mwamanga freezers, champunga mkati, nyama khobwe pambalipa, kwinaku mwayala komba wanu, mnyamata wakatula hair shampoo m'ma Saloon then akukayenda m'makomo ndi bar soap.
Pine gel momwe amayeretsela ku kitchen ma sink ndiku toilet, anthu azichita kukupezani okha pakhomo kuti agule.

Pakutha pa tsiku bwa? Mukalemela aziti mwakhwima, sichoncho?

Adzidzimutseni adani otselelela chaka chino
🀝

Payment details in comment section πŸ‘‡

Register now call or whatssap 0986795267

Use link in comment section πŸ‘‡ to join or Dinan button la whatssaplo mutipeza mwachangu

Kopezeka materials komaso zofunika zonse timakuuzani komaso ma numbers ake ndipo mumakhala mu groupmo mpaka muzakwanitse kupanga zomwe mwaphunzirazo

Remember tikufuna anthu ochepa kuti apange nawo attend osapanga chidodo inu ayi

Inu ndikutitu ndi 5000 kwacha muphunzira zonsezo

Training ya soap ilipo kuyambira pa 7 September not 5 September Tikupepetsa chifukwa chositha date kwa omwe simudalipire...
03/09/2026

Training ya soap ilipo kuyambira pa 7 September not 5 September

Tikupepetsa chifukwa chositha date kwa omwe simudalipire lipirani tikupangeni add

Whatssap us now

Address

Cape Town
0000

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chilungamo Online posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share